Ezekieli 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, idya chakudya ukunjenjemera, ndipo umwe madzi ndi mantha ndiponso nkhawa.+