Ezekieli 16:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndithu ine ndidzakumbukira pangano limene ndinapangana ndi iwe m’masiku a ubwana wako,+ ndipo ndidzakukhazikitsira pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.*+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:60 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
60 Ndithu ine ndidzakumbukira pangano limene ndinapangana ndi iwe m’masiku a ubwana wako,+ ndipo ndidzakukhazikitsira pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.*+