Ezekieli 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Yerusalemu ndipo ulankhule+ kwa malo oyera.+ Ulosere zoipa zimene zidzachitikire dziko la Isiraeli.+
2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Yerusalemu ndipo ulankhule+ kwa malo oyera.+ Ulosere zoipa zimene zidzachitikire dziko la Isiraeli.+