24 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Anthu inu, adani anu adzakugwirani chifukwa chakuti zolakwa zanu zinaululidwa ndipo munachititsa kuti zikumbukiridwe.+ Ndithu adzakugwirani chifukwa machimo anu, kapena kuti zochita zanu zauchimo zinaonekera ndipo simunaiwalidwe.’+