Ezekieli 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, lemba dzina la tsikuli. Ulembe dzina la tsiku lalero. Lero mfumu ya Babulo yazungulira mzinda wa Yerusalemu kuti iuwononge.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:2 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 21
2 “Iwe mwana wa munthu, lemba dzina la tsikuli. Ulembe dzina la tsiku lalero. Lero mfumu ya Babulo yazungulira mzinda wa Yerusalemu kuti iuwononge.+