Ezekieli 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti munawomba m’manja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala ndi mtima wonyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+
6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti munawomba m’manja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala ndi mtima wonyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+