Ezekieli 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzapereka Mowabu limodzi ndi ana a Amoni+ kwa anthu a Kum’mawa+ kuti akhale chuma chawo. Ndidzachita izi kuti ana a Amoni asadzakumbukiridwenso+ pakati pa mitundu ya anthu.
10 Ndidzapereka Mowabu limodzi ndi ana a Amoni+ kwa anthu a Kum’mawa+ kuti akhale chuma chawo. Ndidzachita izi kuti ana a Amoni asadzakumbukiridwenso+ pakati pa mitundu ya anthu.