Ezekieli 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzakulanda chuma chako+ ndi malonda ako.+ Adzagwetsa mpanda wako ndi nyumba zako zosiririka. Miyala yako, zinthu zako zamatabwa ndi fumbi lako, adzaziponya m’madzi.’ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:12 Nsanja ya Olonda,1/1/2008, tsa. 234/15/1988, tsa. 23 Mawu a Mulungu, ptsa. 120-122
12 Iwo adzakulanda chuma chako+ ndi malonda ako.+ Adzagwetsa mpanda wako ndi nyumba zako zosiririka. Miyala yako, zinthu zako zamatabwa ndi fumbi lako, adzaziponya m’madzi.’