Ezekieli 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndikadzakusandutsa mzinda wabwinja ngati mizinda imene simukukhala anthu, ndikadzakubweretsera madzi ambiri, ndipo madzi ochulukawo akadzakumiza,+
19 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndikadzakusandutsa mzinda wabwinja ngati mizinda imene simukukhala anthu, ndikadzakubweretsera madzi ambiri, ndipo madzi ochulukawo akadzakumiza,+