Ezekieli 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu onse ogwiritsa ntchito zopalasira ngalawa, anthu oyendetsa zombo ndi anthu onse ogwira ntchito m’zombo panyanja, adzatuluka m’zombo zawo n’kukaima pamtunda.+
29 Anthu onse ogwiritsa ntchito zopalasira ngalawa, anthu oyendetsa zombo ndi anthu onse ogwira ntchito m’zombo panyanja, adzatuluka m’zombo zawo n’kukaima pamtunda.+