Ezekieli 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,“‘Ndikabweretsa lupanga m’dziko,+ ndipo mogwirizana anthu a m’dzikolo akasankha munthu kuti akhale mlonda wawo,+
2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,“‘Ndikabweretsa lupanga m’dziko,+ ndipo mogwirizana anthu a m’dzikolo akasankha munthu kuti akhale mlonda wawo,+