11 Inde, ndidzachulukitsa anthu ndi nyama+ ndipo adzachulukana ndi kuberekana kwambiri. Ndidzachititsa kuti anthu akhale mwa inu monga momwe zinalili poyamba+ ndipo ndidzakuchitirani zabwino zambiri kuposa poyamba.+ Choncho inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+