4 Tsopano munthuyo anayamba kulankhula nane kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ ona ndi maso ako, imva ndi makutu ako, ndipo uike mtima wako pa zonse zimene ndikuonetse, chifukwa wabweretsedwa kuno kuti ine ndikuonetse zinthu zimenezi. Ukauze nyumba ya Isiraeli zonse zimene uone kuno.”+