Ezekieli 40:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mashelefu oikamo katundu anali chikhatho chimodzi m’lifupi mwawo. Mashelefuwo anawaika kuzungulira khoma lonse lamkati ndipo anawalimbitsa kwambiri. Pamatebulo aja anali kuikapo nyama ya nsembe yoperekedwa monga mphatso.+
43 Mashelefu oikamo katundu anali chikhatho chimodzi m’lifupi mwawo. Mashelefuwo anawaika kuzungulira khoma lonse lamkati ndipo anawalimbitsa kwambiri. Pamatebulo aja anali kuikapo nyama ya nsembe yoperekedwa monga mphatso.+