-
Ezekieli 41:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako analowa m’chipinda chamkati n’kuyamba kuyeza chipilala cham’mbali cha pakhomo ndipo anapeza kuti kuchindikala kwake chinali mikono iwiri. Anayezanso kukula kwa khomo ndipo anapeza kuti linali mikono 6. Kuchokera pakhomo kukafika pakona panali mikono 7.
-