-
Ezekieli 41:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Makomo a zipinda zam’mbali analoza kumpata wa m’mphepete mwa nyumbayo. Khomo limodzi linayang’ana kumpoto lina linayang’ana kum’mwera. Mpata wa m’mphepete mwa nyumbayo unali mikono isanu m’lifupi, kumbali zonse za nyumbayo.
-