-
Ezekieli 41:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Chilichonse panyumbayo chinali ndi muyezo wake. Izi zinali choncho kuyambira pamwamba pa khomo, mkati ndi kunja kwa nyumbayo, khoma lonse kuzungulira mkati mwa nyumbayo ndiponso kunja kwake.
-