Ezekieli 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyeza mafuta oti muzipereka, muzigwiritsa ntchito mtsuko woyezera monga muyezo wanu wa nthawi zonse. Mtsukowo uzikwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa kori.* Mitsuko 10 izikwana homeri chifukwa mitsuko 10 imakwana homeri.
14 Poyeza mafuta oti muzipereka, muzigwiritsa ntchito mtsuko woyezera monga muyezo wanu wa nthawi zonse. Mtsukowo uzikwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa kori.* Mitsuko 10 izikwana homeri chifukwa mitsuko 10 imakwana homeri.