Ezekieli 45:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzichitanso zimenezi pa tsiku la 7 la mweziwo chifukwa cha munthu aliyense amene walakwa komanso chifukwa cha munthu aliyense amene walakwitsa+ zinthu chifukwa chosadziwa. Anthu inu muziperekera Nyumbayi nsembe yophimba machimo.+
20 Muzichitanso zimenezi pa tsiku la 7 la mweziwo chifukwa cha munthu aliyense amene walakwa komanso chifukwa cha munthu aliyense amene walakwitsa+ zinthu chifukwa chosadziwa. Anthu inu muziperekera Nyumbayi nsembe yophimba machimo.+