Ezekieli 48:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuko la Manase+ likhale ndi gawo limodzi. Gawolo liyambire kum’mawa kukafika kumadzulo ndipo lichite malire ndi gawo la fuko la Nafitali.
4 Fuko la Manase+ likhale ndi gawo limodzi. Gawolo liyambire kum’mawa kukafika kumadzulo ndipo lichite malire ndi gawo la fuko la Nafitali.