Danieli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Nebukadinezara anapsa mtima kwambiri+ ndipo analamula kuti abweretse Sadirake, Mesake ndi Abedinego.+ Choncho anabweretsadi amuna amphamvu amenewa pamaso pa mfumu.
13 Pamenepo Nebukadinezara anapsa mtima kwambiri+ ndipo analamula kuti abweretse Sadirake, Mesake ndi Abedinego.+ Choncho anabweretsadi amuna amphamvu amenewa pamaso pa mfumu.