3 M’kupita kwa nthawi, Danieli anaonetsa kuti anali wodziwa kugwira ntchito bwino+ kuposa nduna zonse zapamwamba ndi masatarapi onse, chifukwa anali ndi luso lodabwitsa+ ndipo mfumu inali kuganiza zomukweza kuti akhale pamwamba pa wina aliyense mu ufumuwo.