Danieli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho nduna zapamwamba zimenezi ndi masatarapi aja anapita kwa mfumu ali chigulu.+ Iwo anauza mfumuyo kuti: “Inu mfumu Dariyo, mukhale ndi moyo mpaka kalekale.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Ulosi wa Danieli, tsa. 117
6 Choncho nduna zapamwamba zimenezi ndi masatarapi aja anapita kwa mfumu ali chigulu.+ Iwo anauza mfumuyo kuti: “Inu mfumu Dariyo, mukhale ndi moyo mpaka kalekale.+