Danieli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 Ulosi wa Danieli, ptsa. 119-120
13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+