Danieli 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Itayandikira dzenjelo, inafuulira Danieli ndi mawu achisoni kuti: “Danieli mtumiki wa Mulungu wamoyo, kodi Mulungu wako amene umamutumikira mosalekeza+ wakupulumutsa kwa mikango?”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 126-127 Nsanja ya Olonda,11/15/1996, tsa. 912/1/1988, tsa. 14
20 Itayandikira dzenjelo, inafuulira Danieli ndi mawu achisoni kuti: “Danieli mtumiki wa Mulungu wamoyo, kodi Mulungu wako amene umamutumikira mosalekeza+ wakupulumutsa kwa mikango?”+