Danieli 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho iye anandiuza kuti: “Kodi ukudziwadi kuti n’chifukwa chiyani ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Pamene ndikupita, nayenso kalonga wa Girisi akubwera.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 204-205, 208
20 Choncho iye anandiuza kuti: “Kodi ukudziwadi kuti n’chifukwa chiyani ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Pamene ndikupita, nayenso kalonga wa Girisi akubwera.+