Hoseya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Tsiku la Yehova, ptsa. 57-61 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 22
4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+