Hoseya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inutu mudzachoka chifukwa dzikolo lidzasakazidwa.+ Anthu a ku Iguputo adzakusonkhanitsani pamodzi+ ndipo anthu a ku Mofi+ adzakuikani m’manda. Zomera zoyabwa zidzamera pakatundu wanu wabwino wasiliva.+ M’mahema mwanu mudzamera zitsamba zaminga.+
6 Inutu mudzachoka chifukwa dzikolo lidzasakazidwa.+ Anthu a ku Iguputo adzakusonkhanitsani pamodzi+ ndipo anthu a ku Mofi+ adzakuikani m’manda. Zomera zoyabwa zidzamera pakatundu wanu wabwino wasiliva.+ M’mahema mwanu mudzamera zitsamba zaminga.+