Hoseya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kwambiri kumeneko.+ Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Sindidzapitiriza kuwakonda.+ Akalonga awo onse akuchita makani.+
15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kwambiri kumeneko.+ Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Sindidzapitiriza kuwakonda.+ Akalonga awo onse akuchita makani.+