11 Pa tsiku limene unangoima n’kumaonerera, pa tsiku limene alendo anagwira gulu la asilikali la m’bale wako n’kupita nalo kudziko lina,+ ndiponso pamene alendo enieni analowa pazipata za mzinda wake+ n’kuchita maere pa Yerusalemu,+ iwe unali ngati mmodzi wa adani akewo.