Yona 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo anthuwo anachita mantha kwambiri, ndipo anamufunsa kuti: “Wachitiranji zimenezi?”+ Anthuwo anamufunsa choncho chifukwa anadziwa kuti Yona akuthawa Yehova, pakuti iye anali atawauza zimenezo.
10 Pamenepo anthuwo anachita mantha kwambiri, ndipo anamufunsa kuti: “Wachitiranji zimenezi?”+ Anthuwo anamufunsa choncho chifukwa anadziwa kuti Yona akuthawa Yehova, pakuti iye anali atawauza zimenezo.