Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 12
2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+