Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:18 Tsiku la Yehova, ptsa. 113-114 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 2410/15/1999, ptsa. 15-16
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+