Habakuku 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtunduwu umaseka mafumu monyodola ndipo umaona nduna zapamwamba ngati choseketsa.+ Umasekanso malo alionse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ ndipo umaunjika dothi kenako n’kulanda malowo. Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 11
10 Mtunduwu umaseka mafumu monyodola ndipo umaona nduna zapamwamba ngati choseketsa.+ Umasekanso malo alionse okhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ ndipo umaunjika dothi kenako n’kulanda malowo.