5 Ndiye pakuti vinyo ndi wachinyengo,+ mwamuna wamphamvu amadzimva,+ koma sadzakwaniritsa cholinga chake.+ Iye wakulitsa chilakolako chake ngati Manda ndipo sangakhutire ngati imfa.+ Iye akupitiriza kudzisonkhanitsira mitundu yonse ya anthu ndi anthu onse pamodzi.+