Zefaniya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi imeneyo ndidzaukira onse amene akukuzunza+ ndipo ndidzapulumutsa otsimphina.+ Anthu obalalitsidwa ndidzawasonkhanitsa pamodzi+ ndipo ndidzawachititsa kukhala otamandidwa komanso otchuka m’dziko lonse limene anachititsidwa manyazi.
19 Pa nthawi imeneyo ndidzaukira onse amene akukuzunza+ ndipo ndidzapulumutsa otsimphina.+ Anthu obalalitsidwa ndidzawasonkhanitsa pamodzi+ ndipo ndidzawachititsa kukhala otamandidwa komanso otchuka m’dziko lonse limene anachititsidwa manyazi.