Hagai 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Hagai anafunsanso kuti: “Ngati munthu amene wadetsedwa chifukwa chokhudza mtembo atakhudza chilichonse mwa zinthu zimenezi, kodi chingakhale chodetsedwa?”+ Ansembewo anayankha kuti: “Inde, chingakhale chodetsedwa.”
13 Ndiyeno Hagai anafunsanso kuti: “Ngati munthu amene wadetsedwa chifukwa chokhudza mtembo atakhudza chilichonse mwa zinthu zimenezi, kodi chingakhale chodetsedwa?”+ Ansembewo anayankha kuti: “Inde, chingakhale chodetsedwa.”