Hagai 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Koma tsopano, chonde ganizirani zimenezi mofatsa+ kuyambira lero mpaka m’tsogolo. Ganizirani mmene zinthu zinalili asanasanjikize mwala pamwala unzake m’kachisi wa Yehova.+ Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Nsanja ya Olonda,1/1/1997, ptsa. 17-22
15 “‘Koma tsopano, chonde ganizirani zimenezi mofatsa+ kuyambira lero mpaka m’tsogolo. Ganizirani mmene zinthu zinalili asanasanjikize mwala pamwala unzake m’kachisi wa Yehova.+