Hagai 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu inu, ine ndinawononga mbewu zanu ndi mphepo yotentha,+ matenda a chuku+ ndi matalala.+ Zimenezi zinawononganso ntchito zonse za manja anu.+ Koma panalibe aliyense wa inu amene anabwerera kwa ine,’+ watero Yehova.
17 Anthu inu, ine ndinawononga mbewu zanu ndi mphepo yotentha,+ matenda a chuku+ ndi matalala.+ Zimenezi zinawononganso ntchito zonse za manja anu.+ Koma panalibe aliyense wa inu amene anabwerera kwa ine,’+ watero Yehova.