Zekariya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Unali usiku pamene ndinaona munthu+ atakwera pahatchi* yofiira.+ Iye anaima chilili pakati pa mitengo ya mchisu+ imene inali m’chigwa. Kumbuyo kwake kunali mahatchi ofiirira, ofiira kwambiri ndi oyera.”+
8 “Unali usiku pamene ndinaona munthu+ atakwera pahatchi* yofiira.+ Iye anaima chilili pakati pa mitengo ya mchisu+ imene inali m’chigwa. Kumbuyo kwake kunali mahatchi ofiirira, ofiira kwambiri ndi oyera.”+