Zekariya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno iwo anauza mngelo wa Yehova amene anaima chilili pakati pa mitengo ya mchisu uja kuti: “Ife tayendayenda padziko lapansi+ ndipo taona kuti dziko lonse lapansi langokhala bata popanda chosokoneza.”+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 30
11 Ndiyeno iwo anauza mngelo wa Yehova amene anaima chilili pakati pa mitengo ya mchisu uja kuti: “Ife tayendayenda padziko lapansi+ ndipo taona kuti dziko lonse lapansi langokhala bata popanda chosokoneza.”+