10 “Ukalandire chopereka kuchokera kwa anthu amene anatengedwa kupita kudziko lina.+ Ukalandire choperekacho kwa Heledai, Tobiya ndi Yedaya. Iweyo upite pa tsiku loikidwiratu, ndipo ukalowe m’nyumba ya Yosiya mwana wa Zefaniya,+ kumene kuli anthu ochokera ku Babulowo.