15 Yehova wa makamu adzatchinjiriza anthu ake. Adani awo adzawalasa ndi miyala yoponya ndi gulaye koma iwo adzagonjetsa adaniwo.+ Iwo adzasangalala ndipo adzafuula ngati amwa vinyo.+ Adzadzazidwa ngati mbale zolowa ndiponso ngati mmene magazi amadzazira m’makona a guwa lansembe.+