4 Pa tsiku limenelo,+ ndidzachititsa hatchi+ iliyonse kudabwa kwambiri, ndipo wokwera pahatchiyo ndidzamuchititsa misala.+ Ndidzatsegula maso anga ndi kuyang’ana nyumba ya Yuda,+ ndipo hatchi iliyonse ya anthu a mitundu ina ndidzaichititsa khungu,” watero Yehova.