2 Ndidzasonkhanitsa mitundu yonse ya anthu kuti imenyane ndi Yerusalemu.+ Mzindawu udzalandidwa,+ katundu wa m’nyumba adzatengedwa ndipo akazi adzagwiriridwa.+ Hafu ya anthu a mumzindawu idzatengedwa kupita kudziko lina,+ koma anthu otsala+ sadzachotsedwa mumzindawu.+