Malaki 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mwanena kuti, ‘Chifukwa chiyani?’+ Chifukwa chakuti Yehova wakudzudzulani popeza kuti aliyense wa inu wachitira zachinyengo mkazi amene anamukwatira ali mnyamata,+ ngakhale kuti iye anali mnzake komanso mkazi wa pangano lake.+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 42 Galamukani!,1/2008, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, ptsa. 17-187/1/1989, ptsa. 30-312/1/1989, tsa. 10
14 Inu mwanena kuti, ‘Chifukwa chiyani?’+ Chifukwa chakuti Yehova wakudzudzulani popeza kuti aliyense wa inu wachitira zachinyengo mkazi amene anamukwatira ali mnyamata,+ ngakhale kuti iye anali mnzake komanso mkazi wa pangano lake.+
2:14 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 42 Galamukani!,1/2008, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, ptsa. 17-187/1/1989, ptsa. 30-312/1/1989, tsa. 10