Malaki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, tsa. 284/15/1995, tsa. 23
4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+