Mateyu 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero ngati inuyo, ngakhale kuti ndinu oipa,+ mumadziwa kupereka mphatso zabwino kwa ana anu, kuli bwanji Atate wanu wakumwamba? Ndithudi, iye adzapereka zinthu zabwino+ kwa onse om’pempha! Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, ptsa. 18-195/15/1990, ptsa. 14-15
11 Chotero ngati inuyo, ngakhale kuti ndinu oipa,+ mumadziwa kupereka mphatso zabwino kwa ana anu, kuli bwanji Atate wanu wakumwamba? Ndithudi, iye adzapereka zinthu zabwino+ kwa onse om’pempha!