Mateyu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atatulutsa anthu aja panja, iye analowa ndi kugwira dzanja la mtsikanayo,+ ndipo iye anadzuka.+