Mateyu 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatulutsa chiwandacho, munthu wosalankhulayo analankhula,+ moti khamu la anthulo linadabwa+ ndipo linanena kuti: “Zinthu zoterezi sizinaonekepo n’kale lonse mu Isiraeli.”
33 Atatulutsa chiwandacho, munthu wosalankhulayo analankhula,+ moti khamu la anthulo linadabwa+ ndipo linanena kuti: “Zinthu zoterezi sizinaonekepo n’kale lonse mu Isiraeli.”